E.1 Kuthana ndi moto
Ndondomeko izi zokhudza kuthana ndi moto zikunena njira zabwino kwambiri zothandiza polimbana ndi moto. Mitu yeniyeni ya mu ndondomeko iliyonse ikuyambira p kuyendera dera ndi kulosera momwe moto umayendera ndi kukathera pa kukonza ndi kugwiritsa ntchito dongosolo lothana ndi moto. Uphungu ukuperekedwa p momwe mungapangire ngi kugwiritsa ntchito zipangizo ngati zitafunika kuti mulimbane ndi moto modziteteza komanso momwe mungapangire mikwaso yoyimitsa moto pofuna kuteteza nkhalango ku moto oyambukira.