A.3 Kusamalira chonde m’nthaka
Chonde ndi chofunikira kwambiri pa ulimi.Ndondomekozi zimapereka upangiri pa mmene tingagwiritsire ntchito chonde ndi madzi kuti tipeze zokolola zambiri.Izi zimatukula komanso kusamala dothi kuti tidzagwiritsenso ntchito patsogolo.