C.3 Njira zina zopezera mphamvu ya moto ndi kudalirika kwake

Ndondomeko izi zikupereka malangizo okonzera zipangizo zomwe zimalimbikitsa kugwiritsa ntchito zinthu zomwe zimagwiritsidwa ntchito mobwereza pofuna kupanga mphamvu za magetsi oti agwiritsidwe ntchito pakhomo kapena m’dera m’malo mogwiritsa ntchito nkhuni kapena makala. Ndondomeko izi zikulimbikitsanso kagwiritsidwe ntchito kabwwino ka moto (check energy) ndi kuchepetsa kufuka kwa utsi woyipa omwe umadzetsa mavuto pa umoyo wa anthu komanso kuononga chilengedwe.